NDIMAKUKONDA
この曲の歌詞
Sindidagwepo mchikondi
nkulumbira mbamba ndithu
Ndayendapo ndakazi
zachibwana mbuyomomu
Osadziwa chikondi
chenicheni ndichani
Tsikulina mnakupeza iwe
moyowanga unasintha
Chifundo chako namwali
iwe chinakhudza mtimau
Mzelu zako namwali iwe
zinasuntha mtimau
Liu lako namwali iwe
linatonthoza mtimau
Mtima yathu inalakalaka
kuti tikhale mchikondi
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Sindikufika poti
ndikhale wapamtima pako
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayiwina
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Sindikufika poti
ndikhale wapamtima pako
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayiwina
Tidapangana tsikulina
zokayezetsa magazi
Sindidafune kuononga
wachikondi wangayu
Tidakumana ndadotolo
nkumadikira mayankho
Mtima wanga unagunda
ndinapemphera kolimba
Analankhula dotolo
mulimbemtima mumvere
Magazi anu tayeza
zotsatira ndi izi
Muli nkachilombo
achimwene
koyambitsa edzi hi
Moyo wanga unavuta
kusowa mtengo ogwira
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Ndimakukonda
umandikonda ndiziwa
Mbuyanga chonde
mpatsenikoni mwayi wina
Usalire
ndiwe mbambandedi
Udzapeza wina
mwamuna oposa ine
Anatonthola
mkundiuza kuti
Tizakhala limodzi
mchikondi mpaka muyaya
楽曲情報


CONTENTS
この曲を楽しむ
"NDIMAKUKONDA"のカラオケ配信情報
"NDIMAKUKONDA"の
関連動画
- 「該当データがありません」
"NDIMAKUKONDA"の
#うたスキ動画
- 「該当データがありません」
家庭用カラオケ
- JOYSOUND.comでは著作権保護の観点より、歌詞の印刷行為を禁止しています。
- 都合により、楽曲情報/コンテンツの内容及び配信予定が変更となる場合があります。
- 対応機種が表示されている場合でも、ご利用のシステムによっては選曲できない場合があります。
- リンク先のApple MusicやAmazon Musicのサービス詳細や楽曲の配信状況については各サービスにて十分にご確認ください。
- リンク先のiTunes Storeでご購入される際は商品の内容を十分にご確認ください。
- YouTube動画の表示には[YouTube API]を利用しています。











